Luka 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inenso, popeza kuti ndafufuza zinthu zonse mosamala kwambiri kuchokera pa chiyambi, ndafunitsitsa kuti ndikulembereni mwatsatanetsatane,+ inu wolemekezeka+ koposa, a Teofilo.+ Machitidwe 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 A Teofilo,+ m’nkhani yoyamba ija, ndinalemba zonse zimene Yesu anali kuchita ndi kuphunzitsa kuchokera pa chiyambi,+
3 Inenso, popeza kuti ndafufuza zinthu zonse mosamala kwambiri kuchokera pa chiyambi, ndafunitsitsa kuti ndikulembereni mwatsatanetsatane,+ inu wolemekezeka+ koposa, a Teofilo.+
1 A Teofilo,+ m’nkhani yoyamba ija, ndinalemba zonse zimene Yesu anali kuchita ndi kuphunzitsa kuchokera pa chiyambi,+