Akolose 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Luka,+ dokotala wokondedwa, akuti moni nonse. Dema+ nayenso akuti moni. Filimoni 24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Antchito anzanga, Maliko, Arisitako,+ Dema+ ndi Luka nawonso akupereka moni.