Salimo 39:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ine ndinati: “Ndidzatchinjiriza njira zanga,+Kuti ndisachimwe ndi lilime langa.+Ndidzamanga pakamwa panga kuti patetezeke,+Nthawi zonse pamene woipa ali pamaso panga.”+ Mateyu 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chimene chimalowa m’kamwa sichiipitsa munthu, koma chotuluka m’kamwa mwake n’chimene chimaipitsa munthu.”+ Mateyu 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma zotuluka m’kamwa zimachokera mumtima, ndipo zimenezo zimaipitsa munthu.+ Maliko 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Zoipa zonsezi zimatuluka mkatimo ndipo zimaipitsa munthu.”+
39 Ine ndinati: “Ndidzatchinjiriza njira zanga,+Kuti ndisachimwe ndi lilime langa.+Ndidzamanga pakamwa panga kuti patetezeke,+Nthawi zonse pamene woipa ali pamaso panga.”+
11 Chimene chimalowa m’kamwa sichiipitsa munthu, koma chotuluka m’kamwa mwake n’chimene chimaipitsa munthu.”+