Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Komanso kuti Yehova adzakwaniritse mawu ake okhudza ine amene analankhula,+ akuti, ‘Ana ako+ akadzasamalira njira zawo, mwa kuyenda+ mokhulupirika*+ pamaso panga ndi mtima wawo wonse+ ndi moyo wawo wonse, munthu wa m’banja lako sadzachoka pampando wachifumu wa Isiraeli.’+

  • Salimo 34:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Tetezani lilime lanu ku zinthu zoipa,+

      Ndi milomo yanu kuti isalankhule chinyengo.+

  • Salimo 119:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Kodi wachinyamata+ angakhale bwanji woyera pa moyo wake?

      Mwa kudziyang’anira ndi kuchita zinthu mogwirizana ndi mawu anu.+

  • Aheberi 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiye chifukwa chake n’kofunika kuti tiganizire mozama, kuposa nthawi zonse, zinthu zimene tinamva,+ kuti tisatengeke pang’onopang’ono n’kusiya chikhulupiriro.+

  • 1 Petulo 2:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Pamene anali kunenedwa zachipongwe,+ sanabwezere zachipongwe.+ Pamene anali kuvutika,+ sanawopseze, koma anali kudzipereka kwa iye+ amene amaweruza molungama.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena