Luka 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Komano zogwera panthaka yabwino, ndi anthu amene pambuyo pomva mawuwo ndi mtima woona+ komanso wabwino, amawagwiritsitsa ndi kubereka zipatso mwa kupirira.+ 2 Timoteyo 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Zinthu zimene unazimva kwa ine ndi kwa mboni zambiri+ zokhudza ine, zimenezo uziphunzitse kwa anthu okhulupirika amene nawonso, adzakhala oyenerera bwino kuphunzitsa ena.+
15 Komano zogwera panthaka yabwino, ndi anthu amene pambuyo pomva mawuwo ndi mtima woona+ komanso wabwino, amawagwiritsitsa ndi kubereka zipatso mwa kupirira.+
2 Zinthu zimene unazimva kwa ine ndi kwa mboni zambiri+ zokhudza ine, zimenezo uziphunzitse kwa anthu okhulupirika amene nawonso, adzakhala oyenerera bwino kuphunzitsa ena.+