Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 13:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Mbewu zimene zafesedwa panthaka yabwino, ndi munthu amene wamva mawu ndi kuzindikira tanthauzo lake, amene amabaladi zipatso. Uyu zipatso 100, uyo 60, winayo 30.”+

  • Maliko 4:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Potsirizira pake, zimene zinafesedwa panthaka yabwino, ndiwo anthu amene amamvetsera mawu ndi kuwalandira bwino, ndipo amabala zipatso wina 30, wina 60, ndi wina 100.”+

  • Aheberi 10:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Pakuti mukufunika kupirira,+ kuti mutachita chifuniro cha Mulungu,+ mudzalandire zimene Mulungu walonjeza.+

  • Chivumbulutso 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Popeza unasunga mawu onena za kupirira kwanga,+ inenso ndidzakusunga+ pa ola la kuyesedwa, limene likubwera padziko lonse lapansi kumene kuli anthu. Ndidzakusunga pa ola limene likubwera kudzayesa okhala padziko lapansi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena