Salimo 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndi amene akuyenda mosalakwitsa zinthu,+ amene amachita chilungamo,+Ndi kulankhula zoona mumtima mwake.+ Yohane 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mulungu ndiye Mzimu,+ ndipo onse omulambira ayenera kumulambira motsogoleredwa ndi mzimu ndi choonadi.”+
2 Ndi amene akuyenda mosalakwitsa zinthu,+ amene amachita chilungamo,+Ndi kulankhula zoona mumtima mwake.+
24 Mulungu ndiye Mzimu,+ ndipo onse omulambira ayenera kumulambira motsogoleredwa ndi mzimu ndi choonadi.”+