Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 50:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Amene akupereka nsembe yoyamikira kwa ine ndi amene akundilemekeza.+

      Ndipo amene akuyenda panjirayo motsimikiza,

      Ndidzamuonetsa chipulumutso changa.”+

  • Yesaya 33:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Pali munthu amene amayenda m’chilungamo nthawi zonse,+ amene amalankhula zowongoka,+ amene amakana kupeza phindu mwachinyengo,+ amene salola kuti manja ake alandire chiphuphu,+ amene amatseka makutu ake kuti asamve nkhani zokhudza kukhetsa magazi, ndiponso amene amatseka maso ake kuti asaone zoipa.+

  • Machitidwe 10:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Iye amalandira munthu wochokera mu mtundu uliwonse, amene amamuopa ndi kuchita chilungamo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena