Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 22:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Inu oopa Yehova, m’tamandeni!+

      Inu nonse mbewu ya Yakobo, m’patseni ulemerero!+

      Ndipo muopeni, inu nonse mbewu ya Isiraeli.+

  • Salimo 27:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Pamenepo mutu wanga udzakwezeka pamwamba pa adani onse ondizungulira.+

      Ndipo ndidzapereka nsembe za kufuula mokondwera pahema wake.+

      Ndidzamuimbira nyimbo, ndithu ndidzaimba nyimbo zotamanda Yehova.+

  • Aroma 12:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Chotero ndikukudandaulirani mwa chifundo chachikulu cha Mulungu abale, kuti mupereke matupi anu+ ngati nsembe+ yamoyo,+ yoyera+ ndi yovomerezeka kwa Mulungu,+ ndiyo utumiki wopatulika+ mwa kugwiritsa ntchito luntha la kuganiza.+

  • Aefeso 5:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 m’dzina la Ambuye wathu Yesu Khristu. Nthawi zonse muziyamika+ Mulungu, Atate wathu, pa zinthu zonse.

  • 1 Atesalonika 5:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Muziyamika+ pa chilichonse, pakuti chimenechi ndi chifuniro cha Mulungu kwa inu mwa Khristu Yesu.

  • Aheberi 13:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kudzera mwa iye, tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu. Tizichita zimenezi monga nsembe imene tikupereka kwa Mulungu,+ yomwe ndi chipatso cha milomo yathu.+ Timagwiritsa ntchito milomo imeneyi polengeza dzina lake kwa anthu ena.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena