Salimo 69:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndidzatamanda dzina la Mulungu mwa kuimba nyimbo,+Ndipo ndidzamulemekeza ndi nyimbo zomuyamika.+ Hoseya 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Bwerera kwa Yehova ndi mawu osonyeza kulapa.+ Anthu nonsenu uzani Mulungu kuti, ‘Tikhululukireni zolakwa zathu.+ Landirani zinthu zabwino zochokera kwa ife, ndipo mawu apakamwa pathu akhale ngati ana amphongo a ng’ombe amene tikuwapereka nsembe kwa inu.+ 1 Akorinto 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano ngati ndikulengeza uthenga wabwino,+ chimenechi si chifukwa chodzitamira, pakuti ndinalamulidwa kutero.+ Ndithudi, tsoka+ kwa ine ngati sindilengeza uthenga wabwino!
2 Bwerera kwa Yehova ndi mawu osonyeza kulapa.+ Anthu nonsenu uzani Mulungu kuti, ‘Tikhululukireni zolakwa zathu.+ Landirani zinthu zabwino zochokera kwa ife, ndipo mawu apakamwa pathu akhale ngati ana amphongo a ng’ombe amene tikuwapereka nsembe kwa inu.+
16 Tsopano ngati ndikulengeza uthenga wabwino,+ chimenechi si chifukwa chodzitamira, pakuti ndinalamulidwa kutero.+ Ndithudi, tsoka+ kwa ine ngati sindilengeza uthenga wabwino!