Ekisodo 34:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Wosungira mibadwo masauzande kukoma mtima kosatha,+ wokhululukira zolakwa ndi machimo,+ koma wosalekerera konse wolakwa osam’langa.+ Wolanga ana, zidzukulu, ndi ana a zidzukuluzo chifukwa cha zolakwa za abambo awo.”+ 2 Samueli 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Davide atawerengadi anthuwo anavutika mumtima mwake.+ Choncho Davide anauza Yehova kuti: “Ndachimwa+ kwambiri pochita zimene ndachitazi. Tsopano Yehova, khululukani cholakwa cha ine mtumiki wanu+ chonde, pakuti ndachita chinthu chopusa kwambiri.”+ Salimo 51:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mundisambitse bwinobwino ndi kuchotsa cholakwa changa,+Ndiyeretseni ku tchimo langa.+ Mika 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu+ amene amakhululukira zolakwa+ ndi machimo a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale, pakuti kusonyeza kukoma mtima kosatha kumakusangalatsani.+
7 Wosungira mibadwo masauzande kukoma mtima kosatha,+ wokhululukira zolakwa ndi machimo,+ koma wosalekerera konse wolakwa osam’langa.+ Wolanga ana, zidzukulu, ndi ana a zidzukuluzo chifukwa cha zolakwa za abambo awo.”+
10 Davide atawerengadi anthuwo anavutika mumtima mwake.+ Choncho Davide anauza Yehova kuti: “Ndachimwa+ kwambiri pochita zimene ndachitazi. Tsopano Yehova, khululukani cholakwa cha ine mtumiki wanu+ chonde, pakuti ndachita chinthu chopusa kwambiri.”+
18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu+ amene amakhululukira zolakwa+ ndi machimo a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale, pakuti kusonyeza kukoma mtima kosatha kumakusangalatsani.+