Ekisodo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndi mulungu wina uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+Ndinu woyera kopambana, ndani angafanane ndi inu?+Ndinu woyenera kuopedwa+ ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda.+ Inu ndinu wochita zodabwitsa.+ Salimo 35:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndinene ndi mtima wanga wonse kuti:+“Inu Yehova, ndani angafanane ndi inu,+Amene mumalanditsa wosautsika m’manja mwa munthu wamphamvu kuposa iyeyo,+Amene mumalanditsa wozunzika ndi wosauka m’manja mwa munthu amene akumulanda zinthu zake?”+ Yesaya 40:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi anthu inu Mulungu mungamuyerekezere ndi ndani,+ ndipo kodi mungapange chiyani choti mumufanizire nacho?+
11 Ndi mulungu wina uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+Ndinu woyera kopambana, ndani angafanane ndi inu?+Ndinu woyenera kuopedwa+ ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda.+ Inu ndinu wochita zodabwitsa.+
10 Ndinene ndi mtima wanga wonse kuti:+“Inu Yehova, ndani angafanane ndi inu,+Amene mumalanditsa wosautsika m’manja mwa munthu wamphamvu kuposa iyeyo,+Amene mumalanditsa wozunzika ndi wosauka m’manja mwa munthu amene akumulanda zinthu zake?”+
18 Kodi anthu inu Mulungu mungamuyerekezere ndi ndani,+ ndipo kodi mungapange chiyani choti mumufanizire nacho?+