Salimo 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anandilanditsa kwa mdani wanga wamphamvu,+Anandilanditsa kwa odana nane chifukwa anali amphamvu kuposa ine.+ Salimo 37:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Yehova adzawathandiza ndi kuwapulumutsa.+Adzawapulumutsa kwa anthu oipa ndi kuwalanditsa,+Chifukwa athawira kwa iye.+
17 Anandilanditsa kwa mdani wanga wamphamvu,+Anandilanditsa kwa odana nane chifukwa anali amphamvu kuposa ine.+
40 Yehova adzawathandiza ndi kuwapulumutsa.+Adzawapulumutsa kwa anthu oipa ndi kuwalanditsa,+Chifukwa athawira kwa iye.+