2 Samueli 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anandilanditsa kwa mdani wanga wamphamvu,+Anandilanditsa kwa odana nane chifukwa anali amphamvu kuposa ine.+ Salimo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nyamukani,+ inu Yehova! Ndipulumutseni+ inu Mulungu wanga!+Pakuti mudzakantha adani anga onse pachibwano.+Mano a anthu oipa mudzawaphwanyaphwanya.+
18 Anandilanditsa kwa mdani wanga wamphamvu,+Anandilanditsa kwa odana nane chifukwa anali amphamvu kuposa ine.+
7 Nyamukani,+ inu Yehova! Ndipulumutseni+ inu Mulungu wanga!+Pakuti mudzakantha adani anga onse pachibwano.+Mano a anthu oipa mudzawaphwanyaphwanya.+