Salimo 58:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inu Mulungu, agululeni mano m’kamwa mwawo.+Inu Yehova, thyolani nsagwada za mkango wamphamvu. 2 Atesalonika 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chiweruzo cha Mulunguchi n’cholungama chifukwa akubwezera masautso kwa amene amakusautsani.+