Salimo 35:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Nyamukani ndi kukhala maso kuti mundichitire chilungamo,+Chitani zimenezi inu Mulungu wanga Yehova, kuti muweruze mlandu wanga.+ Yohane 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yesu anati: “Usandikangamire. Pakuti sindinakwerebe kwa Atate. Koma pita kwa abale anga+ ukawauze kuti, ‘Ine ndikukwera kwa Atate+ wanga ndi Atate wanu, kwa Mulungu wanga+ ndi Mulungu wanu.’”+
23 Nyamukani ndi kukhala maso kuti mundichitire chilungamo,+Chitani zimenezi inu Mulungu wanga Yehova, kuti muweruze mlandu wanga.+
17 Yesu anati: “Usandikangamire. Pakuti sindinakwerebe kwa Atate. Koma pita kwa abale anga+ ukawauze kuti, ‘Ine ndikukwera kwa Atate+ wanga ndi Atate wanu, kwa Mulungu wanga+ ndi Mulungu wanu.’”+