Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 22:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndidzalengeza dzina lanu+ kwa abale anga.+

      Ndidzakutamandani pakati pa mpingo.+

  • Mateyu 12:50
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 Pakuti aliyense wochita chifuniro cha Atate wanga wakumwamba, ameneyo ndiye m’bale wanga, mlongo wanga, ndi mayi anga.”

  • Mateyu 25:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Koma poyankha mfumuyo+ idzawauza kuti, ‘Ndithu ndikukuuzani, Pa mlingo umene munachitira zimenezo mmodzi wa abale+ anga aang’ono+ awa, munachitira ine amene.’+

  • Mateyu 28:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kenako Yesu anawauza kuti: “Musaope! Pitani, kauzeni abale anga,+ kuti apite ku Galileya ndipo akandiona kumeneko.”

  • Aroma 8:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Amatero chifukwa amene anawadziwa choyamba+ anawasankhiratu+ kuti adzakhale ofanana+ ndi Mwana wake,+ kuti iye akhale woyamba kubadwa+ pakati pa abale ake ambiri.+

  • Aheberi 2:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pakuti onse, woyeretsayo ndi amene akuyeretsedwawo,+ amachokera kwa mmodzi.+ Pa chifukwa chimenechi, iye sachita manyazi kuwatcha “abale,”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena