Miyambo 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Wokomera mtima munthu wonyozeka akukongoza Yehova,+ ndipo adzam’bwezera zimene anachitazo.+ Mateyu 10:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 “Amene wakulandirani walandiranso ine, ndipo amene walandira ine walandiranso amene anandituma.+ Maliko 9:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Chifukwa aliyense wokupatsani kapu+ ya madzi akumwa chifukwa chakuti ndinu ake a Khristu,+ ndithu ndikukuuzani, ameneyo mphoto yake sidzatayika ayi.
41 Chifukwa aliyense wokupatsani kapu+ ya madzi akumwa chifukwa chakuti ndinu ake a Khristu,+ ndithu ndikukuuzani, ameneyo mphoto yake sidzatayika ayi.