Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 11:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Pali amene amapatsa mowolowa manja, komabe zinthu zake zimawonjezeka.+ Palinso amene safuna kupatsa ena zinthu zoyenera kuwapatsa, koma amangokhala wosowa.+

  • Miyambo 21:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Aliyense wotseka khutu lake kuti asamve kudandaula kwa munthu wonyozeka,+ nayenso adzaitana koma sadzayankhidwa.+

  • Miyambo 28:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Wopatsa zinthu munthu wosauka sadzasowa kanthu,+ koma wophimba maso ake adzapeza matemberero ambiri.+

  • Mateyu 5:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Odala ndi anthu achifundo,+ chifukwa adzachitiridwa chifundo.

  • Mateyu 10:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Amene walandira mneneri chifukwa ndi mneneri adzalandira mphoto yofanana ndi imene mneneri amalandira,+ ndipo amene walandira munthu wolungama chifukwa ndi wolungama adzalandira mphoto yofanana ndi imene munthu wolungama amalandira.+

  • Aheberi 6:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti Mulungu si wosalungama woti angaiwale ntchito yanu ndi chikondi chimene munachisonyeza pa dzina lake,+ mwa kutumikira oyera+ ndipo mukupitiriza kuwatumikira.

  • Yakobo 2:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pakuti wosachita chifundo adzaweruzidwa mopanda chifundo.+ Chifundo n’chopambana kwambiri kuposa chiweruzo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena