-
2 Mafumu 4:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ndiyeno Elisa anauza Gehazi kuti: “Muuze kuti, ‘Mwavutika ndi kutisamalira,+ kodi tingakuchitireni chiyani?+ Kodi pali chinachake choti tikakunenereni kwa mfumu,+ kapena kwa mkulu+ wa asilikali?’” Koma mayiyo anayankha kuti: “Ayi, ndilibe vuto lililonse, chifukwa ndikukhala mwamtendere pakati pa anthu a mtundu wanga.”+
-