Aroma 15:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma tsopano ndatsala pang’ono kupita ku Yerusalemu kukatumikira oyera.+ 2 Akorinto 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ndipo anapitiriza kutipempha mochokera pansi pa mtima ndiponso mochonderera kwambiri, kuti tiwapatse mwayi wopereka nawo mphatso zachifundo ndi kutinso achite nawo utumiki wothandiza oyerawo.+ 2 Timoteyo 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ambuye amulole kukapeza chifundo+ chochokera kwa Yehova m’tsikulo.+ Za utumiki wonse umene anachita ku Efeso, iwe ukuzidziwa bwino.
4 ndipo anapitiriza kutipempha mochokera pansi pa mtima ndiponso mochonderera kwambiri, kuti tiwapatse mwayi wopereka nawo mphatso zachifundo ndi kutinso achite nawo utumiki wothandiza oyerawo.+
18 Ambuye amulole kukapeza chifundo+ chochokera kwa Yehova m’tsikulo.+ Za utumiki wonse umene anachita ku Efeso, iwe ukuzidziwa bwino.