Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 11:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Chotero aliyense wa ophunzirawo, anatsimikiza mtima kutumiza thandizo+ lililonse limene akanatha+ kwa abale okhala ku Yudeya.

  • Machitidwe 19:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Tsopano izi zitatha, Paulo anatsimikiza mumtima mwake kupita ku Yerusalemu,+ kudzera ku Makedoniya+ ndi ku Akaya. Iye anati: “Ndikakafika kumeneko, ndiyeneranso kukaona ku Roma.”+

  • Machitidwe 20:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndipo tsopano, popeza kuti mzimu wandikakamiza,+ ndikupita ku Yerusalemu, ngakhale kuti sindikudziwa zimene zikandichitikire kumeneko.

  • Machitidwe 24:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Choncho pambuyo pa zaka zambiri, ndinabwera kudzapatsa mtundu wanga mphatso zachifundo, ndiponso kudzapereka nsembe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena