Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 25:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 “‘M’bale wanu akasauka pakati panu+ ndipo sangathe kudzisamala, muzim’thandiza.+ Iye ayenera kukhala ndi moyo mmene mlendo wokhala pakati panu+ alili ndi moyo.

  • Miyambo 3:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Usalephere kuchitira zabwino anthu amene akufunikira zabwinozo,+ pamene dzanja lako lingathe kuchita zimenezo.+

  • Machitidwe 24:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Choncho pambuyo pa zaka zambiri, ndinabwera kudzapatsa mtundu wanga mphatso zachifundo, ndiponso kudzapereka nsembe.+

  • Aroma 15:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Abale amene ali ku Makedoniya ndi ku Akaya+ akhala ali ofunitsitsa kupereka+ mphatso kwa oyera osauka a ku Yerusalemu.

  • 1 Akorinto 16:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Tsopano ponena za chopereka+ chopita kwa oyerawo,+ inunso tsatirani malangizo amene ndinapereka ku mipingo ya ku Galatiya.+

  • Agalatiya 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Anangotipempha kuti tizikumbukira aumphawi.+ Ndipo ndayesetsa moona mtima kuchita zimenezi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena