Machitidwe 20:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipo tsopano, popeza kuti mzimu wandikakamiza,+ ndikupita ku Yerusalemu, ngakhale kuti sindikudziwa zimene zikandichitikire kumeneko. Aroma 15:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma tsopano ndatsala pang’ono kupita ku Yerusalemu kukatumikira oyera.+
22 Ndipo tsopano, popeza kuti mzimu wandikakamiza,+ ndikupita ku Yerusalemu, ngakhale kuti sindikudziwa zimene zikandichitikire kumeneko.