Machitidwe 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma tsiku lomwelo usiku, Ambuye anaimirira pambali pake+ ndi kunena kuti: “Limba mtima!+ Pakuti wandichitira umboni mokwanira+ mu Yerusalemu, ndipo ukandichitiranso umboni ku Roma.”+ Aroma 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chotero ndikufunitsitsa kudzalengeza uthenga wabwino+ kwa inunso kumeneko ku Roma.+
11 Koma tsiku lomwelo usiku, Ambuye anaimirira pambali pake+ ndi kunena kuti: “Limba mtima!+ Pakuti wandichitira umboni mokwanira+ mu Yerusalemu, ndipo ukandichitiranso umboni ku Roma.”+