Aroma 15:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma tsopano ndatsala pang’ono kupita ku Yerusalemu kukatumikira oyera.+ 1 Akorinto 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano ponena za chopereka+ chopita kwa oyerawo,+ inunso tsatirani malangizo amene ndinapereka ku mipingo ya ku Galatiya.+ 2 Akorinto 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano ponena za utumiki+ wothandiza oyerawo, n’zosafuna kuti ndichite kukulemberani.
16 Tsopano ponena za chopereka+ chopita kwa oyerawo,+ inunso tsatirani malangizo amene ndinapereka ku mipingo ya ku Galatiya.+