1 Atesalonika 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Timatero pakuti timakumbukira nthawi zonse ntchito zanu zachikhulupiriro,+ ndi ntchito zanu zachikondi. Timateronso pokumbukira mmene munapiririra chifukwa cha chiyembekezo+ chanu mwa Ambuye wathu Yesu Khristu, pamaso pa Mulungu wathu ndi Atate. Aheberi 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Komabe, pitirizani kukumbukira masiku akale. Mutalandira kuwala kochokera kwa Mulungu m’masiku amenewo,+ munapirira mayesero aakulu ndi masautso.+
3 Timatero pakuti timakumbukira nthawi zonse ntchito zanu zachikhulupiriro,+ ndi ntchito zanu zachikondi. Timateronso pokumbukira mmene munapiririra chifukwa cha chiyembekezo+ chanu mwa Ambuye wathu Yesu Khristu, pamaso pa Mulungu wathu ndi Atate.
32 Komabe, pitirizani kukumbukira masiku akale. Mutalandira kuwala kochokera kwa Mulungu m’masiku amenewo,+ munapirira mayesero aakulu ndi masautso.+