Mateyu 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Mukamakhululukira anthu machimo awo, inunso Atate wanu wakumwamba adzakukhululukirani.+ Mateyu 18:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Kodi nawenso sukanam’chitira chifundo+ kapolo mnzako, monga momwe ine ndinakuchitira chifundo?’+ Yakobo 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti wosachita chifundo adzaweruzidwa mopanda chifundo.+ Chifundo n’chopambana kwambiri kuposa chiweruzo.
13 Pakuti wosachita chifundo adzaweruzidwa mopanda chifundo.+ Chifundo n’chopambana kwambiri kuposa chiweruzo.