Mateyu 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mutikhululukire zolakwa* zathu monga mmene ifenso takhululukira amene atilakwira.*+ Mateyu 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Zinthu zonse zimene mukufuna kuti anthu akuchitireni,+ inunso muwachitire zomwezo, pakuti n’zimene Chilamulo ndi Zolemba za aneneri zimafuna.+ Yakobo 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti wosachita chifundo adzaweruzidwa mopanda chifundo.+ Chifundo n’chopambana kwambiri kuposa chiweruzo.
12 “Zinthu zonse zimene mukufuna kuti anthu akuchitireni,+ inunso muwachitire zomwezo, pakuti n’zimene Chilamulo ndi Zolemba za aneneri zimafuna.+
13 Pakuti wosachita chifundo adzaweruzidwa mopanda chifundo.+ Chifundo n’chopambana kwambiri kuposa chiweruzo.