Miyambo 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Aliyense wotseka khutu lake kuti asamve kudandaula kwa munthu wonyozeka,+ nayenso adzaitana koma sadzayankhidwa.+ Yesaya 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsoka kwa anthu oipa! Iwo adzaona zoopsa, chifukwa zimene anachitira ena ndi manja awo, zidzawachitikira iwowo.+ Mateyu 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Odala ndi anthu achifundo,+ chifukwa adzachitiridwa chifundo. Mateyu 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma ngati simukhululukira anthu machimo awo, Atate wanu sadzakukhululukirani machimo anu.+ Luka 6:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pitirizani kukhala achifundo, potengera Atate wanu amenenso ali wachifundo.+
13 Aliyense wotseka khutu lake kuti asamve kudandaula kwa munthu wonyozeka,+ nayenso adzaitana koma sadzayankhidwa.+
11 Tsoka kwa anthu oipa! Iwo adzaona zoopsa, chifukwa zimene anachitira ena ndi manja awo, zidzawachitikira iwowo.+