Mateyu 18:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Mofanana ndi zimenezi,+ Atate wanga wakumwamba adzathana ndi inu ngati aliyense wa inu sakhululukira m’bale wake ndi mtima wonse.”+ Yakobo 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti wosachita chifundo adzaweruzidwa mopanda chifundo.+ Chifundo n’chopambana kwambiri kuposa chiweruzo.
35 Mofanana ndi zimenezi,+ Atate wanga wakumwamba adzathana ndi inu ngati aliyense wa inu sakhululukira m’bale wake ndi mtima wonse.”+
13 Pakuti wosachita chifundo adzaweruzidwa mopanda chifundo.+ Chifundo n’chopambana kwambiri kuposa chiweruzo.