Mateyu 5:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Choncho khalani angwiro, monga mmene Atate wanu wakumwamba alili wangwiro.+ Aefeso 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ndipo yendanibe m’chikondi,+ monganso Khristu anakukondani+ n’kudzipereka yekha chifukwa cha inu. Iye anadzipereka yekha monga chopereka+ ndiponso monga nsembe yafungo lokoma kwa Mulungu.+ Yakobo 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti wosachita chifundo adzaweruzidwa mopanda chifundo.+ Chifundo n’chopambana kwambiri kuposa chiweruzo.
2 ndipo yendanibe m’chikondi,+ monganso Khristu anakukondani+ n’kudzipereka yekha chifukwa cha inu. Iye anadzipereka yekha monga chopereka+ ndiponso monga nsembe yafungo lokoma kwa Mulungu.+
13 Pakuti wosachita chifundo adzaweruzidwa mopanda chifundo.+ Chifundo n’chopambana kwambiri kuposa chiweruzo.