Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Agalatiya 2:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ndinapachikidwa limodzi ndi Khristu.+ Si inenso amene ndikukhala ndi moyo,+ koma Khristu ndi amene akukhala ndi moyo mwa ine.+ Zoonadi, moyo umene ndikukhala tsopano,+ ndikukhala mokhulupirira Mwana wa Mulungu, amene anandikonda ndi kudzipereka yekha chifukwa cha ine.+

  • Aheberi 10:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mwa “chifuniro”+ chimenecho, tayeretsedwa+ kudzera m’thupi la Yesu Khristu loperekedwa nsembe+ kamodzi+ kokha.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena