Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aroma 6:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pakuti tikudziwa kuti umunthu wathu wakale unapachikidwa pamodzi ndi iye pamtengo,+ kuti thupi lathu lauchimo likhale ngati lakufa,+ kuti tisapitirize kukhala akapolo a uchimo.+

  • Agalatiya 5:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Ndiponso anthu amene ali a Khristu Yesu, anapachika thupi lawo pamodzi ndi zikhumbo zake ndi zilakolako zake.+

  • Agalatiya 6:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ineyo sindidzadzitama pa chifukwa china chilichonse, koma chifukwa cha mtengo wozunzikirapo+ wa Ambuye wathu Yesu Khristu basi. Kudzera mwa ameneyu, kwa ine dziko lapansi lapachikidwa, ndipo malinga ndi kuona kwa dziko lapansi,+ ineyo ndapachikidwa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena