Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 25:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Koma poyankha mfumuyo+ idzawauza kuti, ‘Ndithu ndikukuuzani, Pa mlingo umene munachitira zimenezo mmodzi wa abale+ anga aang’ono+ awa, munachitira ine amene.’+

  • Luka 10:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Amene akukumverani,+ akumveranso ine. Ndipo amene akunyalanyaza+ inu akunyalanyazanso ine. Ndipotu amene akunyalanyaza ine akunyalanyazanso amene anandituma.”

  • Yohane 12:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Koma Yesu anafuula kuti: “Wokhulupirira ine sakhulupirira ine ndekha, komanso amakhulupirira iye amene anandituma ine.+

  • Yohane 13:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ndithudi ndikukuuzani, Wolandira aliyense amene ine ndamutuma walandiranso ine.+ Ndipo amene walandira ine, walandiranso amene anandituma.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena