Mateyu 10:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 “Amene wakulandirani walandiranso ine, ndipo amene walandira ine walandiranso amene anandituma.+ Maliko 9:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 “Aliyense wolandira mmodzi wa ana aang’ono oterewa m’dzina langa, walandiranso ine. Ndipo aliyense wolandira ine, salandira ine ndekha, koma amalandiranso iye amene anandituma.”+ Yohane 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 kuti onse alemekeze Mwana+ monga mmene amalemekezera Atate. Wosalemekeza Mwana salemekeza Atate amene anamutuma.+ Yohane 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndithudi ndikukuuzani, Wolandira aliyense amene ine ndamutuma walandiranso ine.+ Ndipo amene walandira ine, walandiranso amene anandituma.”+
37 “Aliyense wolandira mmodzi wa ana aang’ono oterewa m’dzina langa, walandiranso ine. Ndipo aliyense wolandira ine, salandira ine ndekha, koma amalandiranso iye amene anandituma.”+
23 kuti onse alemekeze Mwana+ monga mmene amalemekezera Atate. Wosalemekeza Mwana salemekeza Atate amene anamutuma.+
20 Ndithudi ndikukuuzani, Wolandira aliyense amene ine ndamutuma walandiranso ine.+ Ndipo amene walandira ine, walandiranso amene anandituma.”+