Yohane 3:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Atate amakonda Mwana wake+ ndipo anapereka zinthu zonse m’manja mwake.+ Afilipi 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anachita zimenezi kuti m’dzina la Yesu, onse akumwamba, apadziko lapansi, ndi apansi pa nthaka apinde mawondo awo.+
10 Anachita zimenezi kuti m’dzina la Yesu, onse akumwamba, apadziko lapansi, ndi apansi pa nthaka apinde mawondo awo.+