Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 16:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndiyeno Mose anapitiriza kuti: “Mudzaona zimenezi Yehova akakupatsani nyama yoti mudye madzulo ano, ndi mkate wokwanira m’mawa, chifukwa Yehova wamva kung’ung’udza kwanu kumene mukum’ng’ung’udzira. Ife ndife ndani? Kung’ung’udza kwanu si kotsutsana ndi ife, koma n’kotsutsana ndi Yehova.”+

  • Yohane 12:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Aliyense wondinyalanyaza ndi kusalandira mawu anga, ali naye mmodzi womuweruza. Mawu+ amene ine ndalankhula ndi amene adzamuweruze pa tsiku lomaliza.

  • Yohane 15:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Wodana ndi ine amadananso ndi Atate wanga.+

  • 1 Atesalonika 4:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Choncho munthu wonyalanyaza+ chiphunzitso chimenechi sakunyalanyaza munthu, koma Mulungu+ amene amaika mzimu wake woyera+ mwa inu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena