Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 21:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Anthuwo ataona zimenezo, anapita kwa Mose n’kumuuza kuti: “Tachimwa ife,+ chifukwa talankhula mowiringula kwa Yehova ndiponso kwa inuyo. Tipepesereni kwa Yehova kuti atichotsere njokazi.”+ Pamenepo Mose anayamba kuwapepesera kwa Mulungu.+

  • 1 Samueli 8:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Poyankha, Yehova anauza Samueli+ kuti: “Mvera zonse zimene anthuwo akunena kwa iwe,+ pakuti sanakane iweyo koma akana ine kuti ndisakhale mfumu yawo.+

  • Yesaya 32:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 pakuti munthu wopusa adzalankhula zinthu zopanda nzeru,+ ndipo mtima wake udzaganiza zochita zinthu zopweteka ena.+ Iye adzachita zimenezi kuti azichita zopanduka,+ kuti azinenera Yehova zoipa, kuti achititse mimba ya munthu wanjala kukhala yopanda kanthu,+ ndiponso kuti achititse munthu waludzu kukhala wopanda chilichonse choti amwe.

  • Luka 10:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Amene akukumverani,+ akumveranso ine. Ndipo amene akunyalanyaza+ inu akunyalanyazanso ine. Ndipotu amene akunyalanyaza ine akunyalanyazanso amene anandituma.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena