1 Samueli 24:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwambi wa anthu akale umati, ‘Choipa chimachokera kwa munthu woipa,’+ koma dzanja langali silidzakukhudzani. Salimo 58:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ayi! Inu mukuchita zosalungama padziko lapansi mogwirizana ndi zimene mtima wanu ukufuna,+Ndipo mukukonza njira zochitira chiwawa ndi manja anu.+ Mika 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Tsoka kwa anthu amene amati akagona pabedi, amakonza chiwembu ndiponso kuganiza mmene angachitire zoipa.+ M’mawa kukangocha, iwo amazichitadi+ chifukwa chakuti ali ndi mphamvu zochitira zimenezo.+
13 Mwambi wa anthu akale umati, ‘Choipa chimachokera kwa munthu woipa,’+ koma dzanja langali silidzakukhudzani.
2 Ayi! Inu mukuchita zosalungama padziko lapansi mogwirizana ndi zimene mtima wanu ukufuna,+Ndipo mukukonza njira zochitira chiwawa ndi manja anu.+
2 “Tsoka kwa anthu amene amati akagona pabedi, amakonza chiwembu ndiponso kuganiza mmene angachitire zoipa.+ M’mawa kukangocha, iwo amazichitadi+ chifukwa chakuti ali ndi mphamvu zochitira zimenezo.+