Salimo 94:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kodi inu mudzagwirizana ndi olamulira ankhanza,+Pamene akuyambitsa mavuto mwa kupanga malamulo?+ Yesaya 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsoka kwa amene akukhazikitsa malamulo oipa,+ ndi kwa amene amangokhalira kulemba malamulo obweretsa mavuto kwa anthu.
10 Tsoka kwa amene akukhazikitsa malamulo oipa,+ ndi kwa amene amangokhalira kulemba malamulo obweretsa mavuto kwa anthu.