Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 21:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiyeno mupeze anthu awiri+ opanda pake+ adzakhale patsogolo pake ndi kupereka umboni wotsutsana naye.+ Adzanene kuti, ‘Iwe watemberera Mulungu ndi mfumu!’+ Kenako mukamutulutse kunja ndi kum’ponya miyala kuti afe.”+

  • Salimo 58:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Ayi! Inu mukuchita zosalungama padziko lapansi mogwirizana ndi zimene mtima wanu ukufuna,+

      Ndipo mukukonza njira zochitira chiwawa ndi manja anu.+

  • Yesaya 10:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tsoka kwa amene akukhazikitsa malamulo oipa,+ ndi kwa amene amangokhalira kulemba malamulo obweretsa mavuto kwa anthu.

  • Danieli 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mukangomva kulira kwa lipenga, chitoliro, zeze wamng’ono, zoimbira zosiyanasiyana za zingwe, chitoliro chathumba ndi zipangizo zosiyanasiyana zoimbira,+ mugwade ndi kuwerama mpaka nkhope zanu pansi ndi kulambira fano lagolide limene mfumu Nebukadinezara yaimika.

  • Danieli 6:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Nduna zonse zapamwamba za mu ufumu uno, akuluakulu a boma, masatarapi, alangizi a mfumu, ndi abwanamkubwa agwirizana kuti inu mfumu mukhazikitse lamulo+ loletsa munthu aliyense kupemphera kwa mulungu kapena kwa munthu wina aliyense kwa masiku 30, kupatulapo kwa inu nokha mfumu. Aliyense amene samvera lamulo limeneli aponyedwe m’dzenje la mikango.+

  • Machitidwe 5:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 kuti: “Tinakulamulani mwamphamvu+ kuti musadzaphunzitsenso m’dzina limeneli, koma taonani tsopano! Mwadzaza Yerusalemu yense ndi chiphunzitso chanuchi,+ ndipo mwatsimikiza mtima ndithu kuti mubweretse magazi+ a munthu ameneyu pa ife.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena