Salimo 59:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti, taonani! Iwo akundidikirira kuti awononge moyo wanga.+Inu Yehova, anthu amphamvu akundiukira,+Ngakhale kuti ine sindinapanduke kapena kuchita tchimo lililonse.+ Salimo 94:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kodi inu mudzagwirizana ndi olamulira ankhanza,+Pamene akuyambitsa mavuto mwa kupanga malamulo?+
3 Pakuti, taonani! Iwo akundidikirira kuti awononge moyo wanga.+Inu Yehova, anthu amphamvu akundiukira,+Ngakhale kuti ine sindinapanduke kapena kuchita tchimo lililonse.+