Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 19:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Patapita nthawi, Sauli anauza mwana wake Yonatani ndi atumiki ake onse kuti akufuna kupha Davide.+

  • Salimo 10:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Amadikirira anthu pamalo obisika ngati mkango pamalo ake obisalapo.+

      Amawadikirira+ kuti atenge mokakamiza munthu wosautsika.

      Amakulunga wosautsika mu ukonde wake ndi kumutenga mokakamiza.+

  • Salimo 37:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Woipa amalondalonda munthu wolungama,+

      Ndipo amafuna kuti amuphe.+

  • Salimo 38:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Anthu amene akufuna kundiwononga anditchera misampha,+

      Amene akufuna kundivulaza akulankhula motsutsana nane,+

      Ndipo amakhala akukonza zachinyengo tsiku lonse.+

  • Salimo 56:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Amandiukira ndi kundibisalira,+

      Iwo nthawi zonse amaonetsetsa mmene ndikuyendera,+

      Pamene akundidikirira kuti awononge moyo wanga.+

  • Salimo 71:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti adani anga anena za ine,+

      Ndipo anthu olondalonda moyo wanga, onse pamodzi achita upo,+

  • Yohane 7:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Zimenezi zitatha, Yesu anapitiriza kuyendayenda mu Galileya. Iye sanafune kumayendayenda mu Yudeya, chifukwa Ayuda anali kufunitsitsa kumupha.+

  • Machitidwe 23:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Koma chonde musalole kuti akunyengerereni, pakuti amuna oposa 40 akumudikirira panjira.+ Amenewa achita kulumbira modzitemberera kuti sadya kapena kumwa kanthu kufikira atamupha.+ Moti panopa akonzeka, akungoyembekezera chilolezo chanu.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena