Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 10:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Amadikirira anthu pamalo obisika ngati mkango pamalo ake obisalapo.+

      Amawadikirira+ kuti atenge mokakamiza munthu wosautsika.

      Amakulunga wosautsika mu ukonde wake ndi kumutenga mokakamiza.+

  • Miyambo 1:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Chifukwa mapazi awo amathamangira zoipa,+ ndipo iwo amafulumira kukakhetsa magazi.+

  • Yesaya 59:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mapazi awo amangothamangira kukachita zoipa,+ ndipo amafulumira kuti akakhetse magazi osalakwa.+ Maganizo awo ndi opweteka anzawo.+ M’misewu mwawo amangokhalira kusakazana ndi kuwonongana.+

  • Machitidwe 9:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Tsopano patapita masiku ambiri, Ayudawo anasonkhana pamodzi ndi kupangana zoti amuphe.+

  • 2 Akorinto 11:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Pa maulendo kawirikawiri, zoopsa za m’mitsinje, zoopsa za achifwamba pamsewu,+ zoopsa zochokera kwa anthu a mtundu wanga,+ zoopsa zochokera kwa anthu a mitundu ina,+ zoopsa mumzinda,+ zoopsa m’chipululu, zoopsa za panyanja, zoopsa pakati pa abale onyenga,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena