Salimo 58:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ayi! Inu mukuchita zosalungama padziko lapansi mogwirizana ndi zimene mtima wanu ukufuna,+Ndipo mukukonza njira zochitira chiwawa ndi manja anu.+ Aroma 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Kusakaza ndi kusautsa kuli m’njira zawo,+
2 Ayi! Inu mukuchita zosalungama padziko lapansi mogwirizana ndi zimene mtima wanu ukufuna,+Ndipo mukukonza njira zochitira chiwawa ndi manja anu.+