Yesaya 59:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mapazi awo amangothamangira kukachita zoipa,+ ndipo amafulumira kuti akakhetse magazi osalakwa.+ Maganizo awo ndi opweteka anzawo.+ M’misewu mwawo amangokhalira kusakazana ndi kuwonongana.+
7 Mapazi awo amangothamangira kukachita zoipa,+ ndipo amafulumira kuti akakhetse magazi osalakwa.+ Maganizo awo ndi opweteka anzawo.+ M’misewu mwawo amangokhalira kusakazana ndi kuwonongana.+