Machitidwe 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mkanganowo utakula kwambiri, mkulu wa asilikali anachita mantha kuti anthuwo amukhadzulakhadzula Paulo. Chotero analamula asilikali+ kuti apite komweko kuti akamuchotse pakati pawo ndi kumubweretsa kumpanda wa asilikali.+
10 Mkanganowo utakula kwambiri, mkulu wa asilikali anachita mantha kuti anthuwo amukhadzulakhadzula Paulo. Chotero analamula asilikali+ kuti apite komweko kuti akamuchotse pakati pawo ndi kumubweretsa kumpanda wa asilikali.+