Machitidwe 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 mkulu wa asilikali analamula kuti alowe naye kumpanda wa asilikali. Iye anati ayenera kumufunsa mafunso kwinaku akumukwapula, kuti adziwe bwino chimene chachititsa kuti anthu amukuwize+ choncho.
24 mkulu wa asilikali analamula kuti alowe naye kumpanda wa asilikali. Iye anati ayenera kumufunsa mafunso kwinaku akumukwapula, kuti adziwe bwino chimene chachititsa kuti anthu amukuwize+ choncho.