Machitidwe 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atakhala kumeneko miyezi itatu, anaganiza zobwerera ku Makedoniya, chifukwa chakuti Ayuda anamukonzera chiwembu.+ Chiwembuchi anachikonza Paulo atangotsala pang’ono kuyamba ulendo wa pamadzi wopita ku Siriya. Machitidwe 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kutacha, Ayuda anakonza chiwembu+ ndi kulumbira mwa kudzitemberera+ kuti sadya kapena kumwa kanthu kufikira atapha Paulo.+ 2 Akorinto 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndi atumiki a Khristu kapena? Ndikuyankha ngati wamisala, ineyo ndiye weniweni woposanso iwowo:+ m’ntchito zovuta mowirikiza koposa,+ m’ndende osachita kunena,+ kumenyedwa kosawerengeka, kutsala pang’ono kufa kawirikawiri.+
3 Atakhala kumeneko miyezi itatu, anaganiza zobwerera ku Makedoniya, chifukwa chakuti Ayuda anamukonzera chiwembu.+ Chiwembuchi anachikonza Paulo atangotsala pang’ono kuyamba ulendo wa pamadzi wopita ku Siriya.
12 Kutacha, Ayuda anakonza chiwembu+ ndi kulumbira mwa kudzitemberera+ kuti sadya kapena kumwa kanthu kufikira atapha Paulo.+
23 Ndi atumiki a Khristu kapena? Ndikuyankha ngati wamisala, ineyo ndiye weniweni woposanso iwowo:+ m’ntchito zovuta mowirikiza koposa,+ m’ndende osachita kunena,+ kumenyedwa kosawerengeka, kutsala pang’ono kufa kawirikawiri.+